Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Zinasitha Vibes 1 by Cee

SongGPT
Zinasitha Vibes 1 by Cee - Amapiano Log Drum,Both Vocals music cover art

Zinasitha Vibes 1

Amapiano Log Drum,Both Vocals

0:003:42
Lyrics
Description
(intro)
komatu eeeeh eeeeh I can
sakudziwa zinasitha nyengo zanga zinasitha
(verse)
sakudziwa zinasitha nyengo zanga zinasitha, eti kunditchera minga akufuna kutamika
ngati mukufuna thandizo
mudzandifunse kapena
mwina mufuna tipuse,
eya tavomera , inuyo ndi
Doro ifeyo ndikape nanga
bwanji mukufuna ngini zifanane
ndikuuzeni miyala mukugendayo
ndikutola ndimangila nyumba
(kolassi);
ma gay gwilani brake apo bii mugwidwatu heart break
ma gay paliwilo kundithamangila koma sakudziwa nyengo zanga zinasitha nyengo zanga zinasitha, mmmh mmmh
zinasitha,
zinasitha,
zinasitha, eeeh eeeh eeeh