Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Uziyamika — A Prayerful Awakening 1 by Shafie

SongGPT
Uziyamika — A Prayerful Awakening 1 by Shafie - Gospel music cover art

Uziyamika — A Prayerful Awakening 1

Gospel

0:002:53
Lyrics
Description
[Verse 1]
Allah watizusa, alhamdulillah
Tikutumikira dziko loti leni
Siphokoso latambala, timbale wadzukanalo
Komwe ndi chifunilo cha namalenga
Sikupambana kwathu, nchikonzelo chake
Kukatichela tizingiyamika
Pochita chifunilo chake
Polingalira moyo wathu,
Pomwetafikira lelo
Sitiziwammawatifikila
Pomwe kwatichela lelo
Sitiziwa chizulo kutidela
[Chorus]
Salida nthawi yako (vocals baking), nthawi yako
Samalisa tsiku lalo
(vocals baking) Tsiku lalo
(majority vocals) Allah akakuzusa uziyamika
Nkusamalisa nthawi yomwe wapasidwa
Nkusowa zomse zomwe walakwisa
Kuti wa Allah ukakhale owina
[Verse 2]
Dzuwa latuluka mpakana lalowa
Tilibe ndimoyo, alhamdulillah
Kodi ndichani chomwe tasogoza kwa Allah
Munthawi yomwe sizabwelela
Nangandichanichomwe chikuza pammawa
Kodi tili okonzeka kuchilandila?
(vocals fans) Gwilantchito ya Allah, yo ngatipambuyo pake
Owona imfa, usamale
Imfayi ndilonjezo, ukonzekele eya
Uziwelengesele zoyipa zomwe uchita ubwelele
(majority vocals) Yaibuni Adam, usaiwale imfa
Poti imfayo, simakuiwala
[Bridge]
Nde usamalise
Usamale yeye yeye
[Chorus]
Salida nthawi yako (vocals baking), nthawi yako
Samalisa tsiku lalo
(vocals baking) Tsiku lalo
(majority vocals) Allah akakuzusa uziyamika
Nkusamalisa nthawi yomwe wapasidwa
Nkusowa zomse zomwe walakwisa
Kuti wa Allah ukakhale owina
[Outro]
Time given, don’t waste the shadows
Step gentle where your breath lands
Every dawn whispers the chance to praise
Hold fast, for the night waits