Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Sankhani Sabata la Yehova 1 by Solomon

SongGPT
Sankhani Sabata la Yehova 1 by Solomon - Gospel,Mixed Choir Vocals music cover art

Sankhani Sabata la Yehova 1

Gospel,Mixed Choir Vocals

0:003:53
Lyrics
Description
🎶 INTRO – (Soft, reverent – single voice or light harmony)
> "Sankhani Yesu, Ambuye — mwini tsiku la Sabata,
Yemwe ndi Njira ya Moyo wosatha..."
---
🎶 VERSE 1 – (Choir builds in harmony)
🎵 Nthawi yoletsa kugula ndi kugulitsa ija nde yafika.
Lamulo latsopano laikidwa,
Aliyense akakamizidwa
Kuti adzipuma Sunday.
🎶 Koma omwe akana kusunga Sunday
Kumasunga Sabata la Yehova Mulungu Mlengi,
Aziphedwa, komanso sazikhoza kugula ndi kugulitsa.
🎵 Koma kodi Mawu a Mulungu akunena chiyani?
Masiku asanu ndi limodzi
Udzigwira ntchito zako zonse...
🎶 ...ndikumaliza ndiponso kupumula
Tsiku lachisanu ndi chiwiri —
Monga Iye mwini adachitira.
🎶 Adamaliza ntchito yonse yolenga,
Ndipo adapumula tsiku lachisanu ndi chiwiri — Sabata!
---
🎶 CHORUS – (Full choir, strong harmony & power)
🎵 Sabata la Ambuye laiwalika,
Anthu ambiri akusunga Sunday,
Kusiya Sabata la Yehova.
🎶 Usankha Mulungu, posunga Sabata lake (Saturday)?
Kapena uvomera kumvera Satana, posunga Sunday?
🎵 Sankhani Sabata la Yehova!
🎶 Sankhani Yesu, Ambuye — mwini tsiku la Sabata,
Yemwe ndi Njira ya Moyo wosatha.
---
🎶 BRIDGE – (Strong, unison or tight harmony)
🎶 Sunday ndi lemba la chilombo — (Six, six, six)
Sabata ndi chizindikiro cha Mulungu.
🎶 Usasinthe Choonadi!
Sankhani Yesu, Ambuye — mwini tsiku la Sabata,
Yemwe ndi Njira ya Moyo wosatha.
🎵 Sankhani Sabata, la Mulungu Mlengi —
Chizindikiro cha Mulungu ndi Anthu — Osati Sunday!
---
🎶 VERSE 2 – (Choir builds in harmony)
🎼 Khalani ngati Shadraki, Meshaki ndi Abedinego!
🎵 Anakakamizidwa kulambira fano,
Koma sanagonjere lamulo la mfumu —
Anaima njii — kumvera Mulungu!
🎶 Nthawi yakwananso,
Kuti aliyense akakamizidwe kusunga Sunday
Monga zinachitikira mu three hundred and twenty one A.D.,
Pamene Constantine anaika lamulo...
🎵 ...Kuti aliyese adzipumula Sunday,
Ndipo okana — amkaphedwa.
🎶 Sunday ndi lemba la chilombo — (six, six, six)
Sabata ndi chizindikiro cha Mulungu ndi anthu!
🎶 Sankhani Yesu, Ambuye — mwini tsiku la Sabata,
Yemwe ndi Njira ya Moyo wosatha!
---
🎶 CHORUS – REPEAT (With more power & emotion)
🎵 Sabata la Ambuye laiwalika,
Anthu ambiri akusunga Sunday,
Kusiya Sabata la Yehova...
🎶 Usankha Mulungu, posunga Sabata lake (Saturday)?
Kapena uvomera kumvera Satana, posunga Sunday (666)?
🎶 Sankhani Sabata la Mulungu Mlengi —
Chizindikiro cha Mulungu ndi Anthu — Osati Sunday!
---
🎶 OUTRO – (Choir soft but firm – harmonic layers)
🎶 Sankhani Yesu, Ambuye — mwini tsiku la Sabata,
Yemwe ndi Njira ya Moyo wosatha...
🎶 Sankhani Sabata, la Mulungu Mlengi
Chizindikiro cha Mulungu ndi Anthu — Osati Sunday...
> (Fade out with light piano and guitar arpeggio)