Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Ntundu wa Ntolokonyo 2 by Ras

SongGPT
Ntundu wa Ntolokonyo 2 by Ras - roots reggae music cover art

Ntundu wa Ntolokonyo 2

roots reggae

0:003:00
Lyrics
Description
[Chorus]
Ankwele tigwilizane
A kafileni tigwilizane
A nzunga tigwilizane
A khilise tigwilizane
Ana Tonse tigwilizane, vansei
Tonse ndife Ntundu wa Ntolokonyo
Tikayambana tiyeni tikambilane
Monga anthu a modzi
Ngati mukuyamba ndinu akulu akulu
Anafe tithawile kuti?
Ine Junior kuno Julia
[Chorus]
Ankwele tigwilizane
A kafileni tigwilizane
A nzunga tigwilizane
A khilise tigwilizane
Ana Tonse tigwilizane, vansei
[Verse]
Ndidziwa munthu amalakwitsa
Zikalakwika tibwele pamodzi
Tikambilane
Tigonjelane
Tilolelane
Ine Junior kuno kulila a a a!
[Bridge]
Ya, ine Junior kuno kulila
Kulilila Ntundu wanga
Wa Ntolokonyo, mm mm
Ras Hezron once again
Represent Nchalo Gettoh
[Chorus]
Ankwele tigwilizane
A kafileni tigwilizane
A nzunga tigwilizane
A khilise tigwilizane
Ana Tonse tigwilizane, vansei
Tonse ndife Ntundu wa Ntolokonyo
[Outro]
Tigwilizane, vansei
Ntundu wa Ntolokonyo