Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Lowetsa Yesu Mu Mtima 2 by Gift

SongGPT
Lowetsa Yesu Mu Mtima 2 by Gift - Gospel Folk,Female Vocals music cover art

Lowetsa Yesu Mu Mtima 2

Gospel Folk,Female Vocals

0:003:46
Lyrics
Description
[Verse 1]
Kodi watopa nazo zoipa,
Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ngati ufuna kutembenuka,
Lowetsa Yesu mu Mtima.
[Chorus]
Leka kukayikatu;
Usamkanenso lero,
Tsegula Mtima wako;
Lowetsa Yesu mu Mtima.
[Verse 2]
Ukafuna kukhala woyera,
Lowetsa Yesu mu Mtima;
Madzi osamba ali pafupi,
Lowetsa Yesu mu Mtima.
[Verse 3]
Ngati muli bvuto mtimamo,
Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ngati wapereweza za m’dziko,
Lowetsa Yesu mu Mtima.
[Verse 4]
Abwenzi akakusandukira,
Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ndiye bwenzi losatekeseka,
Lowetsa Yesu mu Mtima.
[Verse 5]
Ngati uyimba nao odala,
Lowetsa Yesu mu Mtima;
Udzalowe m’nyumba za mpumulo,
Lowetsa Yesu mu Mtima.
[Chorus]
Leka kukayikatu;
Usamkanenso lero,
Ndatsegula citseko,
Kuti Yesu alowemo.