Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Kuyesa Ndikuyesa (Trying and Trying) 2 by Wilfred

SongGPT
Kuyesa Ndikuyesa (Trying and Trying) 2 by Wilfred - roots reggae music cover art

Kuyesa Ndikuyesa (Trying and Trying) 2

roots reggae

0:003:00
Lyrics
Description
[Intro]
Roots reggae
Nchito ndikugwira, masana ndi usikuu
Koma phindu Lake, ine sindiliona
Pali mabwana ena, amalemba wantchito
Koma mwezi ukamatha, malipiro sawapatsa
Tsono inu mukandiona, nditangovala nsanza
Mumayamba Kundinyoza
Ena munditcha wamisala ena ena munditcha Opanda nzeeru
Koma mudziwe
[Chorus]
Kuyesa ndikuyesa, koma zinthu Zingovuta, yes Zingovuta!!
Ndimagwila nchito kuyambila m,mamawa, mpakana madzulo, osapuma Ayi
Kuyesa ndikuyesa, koma zinthu Zingovuta, yes Zingovuta!!
Ndimagwila nchito kuyambila m,mamawa, mpakana madzulo, osapuma Ayi
[Verse]
Vansei, ndimagwila nchito, kuyambila m,mamawa, mpakana madzulo ine osapuma
Kuchita kusowa nthawi yodyako nsima
Madzulo ndikaweluka mpamene ndimakadya Dina
[Chorus]
Kuyesa ndikuyesa, koma zinthu Zingovuta, yes Zingovuta!!
Ndimagwila nchito kuyambila m,mamawa, mpakana madzulo, osapuma Ayi
Kuyesa ndikuyesa, koma zinthu Zingovuta, yes Zingovuta
Ndimagwila nchito kuyambila m,mamawa, mpakana madzulo, osapuma Ayi
[Outro]
It's Ras Hezron once again, represent Nchalo Gettoh, Fire