Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Kuyesa Ndikuyesa (I Keep Trying) 2 by Wilfred

SongGPT
Kuyesa Ndikuyesa (I Keep Trying) 2 by Wilfred - reggae dancehall music cover art

Kuyesa Ndikuyesa (I Keep Trying) 2

reggae dancehall

0:002:56
Lyrics
Description
[Verse 1]
Ntchito ndikugwiraai, masana ndi usikuu, koma phindu Lake ine sindiliona alidyela ndi anthu enaa, pali mabwana enaa, amalemba wantchito, koma mwezi ukamatha, malipiro sawapatsa, amawapondelezaa, tsono inu mukandiona, nditangovala nsanza, mumayamba Kundinyozaa, Ena munditcha wamisala ena munditcha Opanda nzeeru, koma mudziwe
[Chorus]
Kuyesa ndikuyesa aai, koma zinthu Zingovuta Ai, poti ndimagwila nchito kuyambila m,mamawa, mpakana madzuloo osapuma
Kuyesa ndikuyesa aai, koma zinthu Zingovuta Ai, poti ndimagwila nchito kuyambila m,mamawa mpakana madzuloo, osapuma Ayi
[Verse 2]
Ndimagwila nchito kuyambila m,mamawa, mpakana madzulo ndithu osapuma, kuchita kusowa nthawi yoti nkudyako nsima, madzulo ndikaweluka mpamene ndimakadya Dina, ndi Ntchito Yanga ija yodziwika bwino ya ulonda, usiku onse umathela nditangovala, ndinaiwa kale zoti anthu amadya Dina, m,mamawa kukacha ndimangodya kadzutsa, tcheche
[Chorus]
Kuyesa ndikuyesa aai, koma zinthu Zingovuta Ai, poti ndimagwila nchito kuyambila m,mamawa, mpakana madzuloo osapuma Ayi
Kuyesa ndikuyesa aai, koma zinthu Zingovuta Ai, poti ndimagwila nchito kuyambila m,mamawa mpakana madzuloo, osapuma Ayi
[Bridge]
Osapuma Ayi, osapuma Ayi, osapuma Ayi
[Outro]
It's Ras Hezron once again