Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Kuwala Kwako (Your Light) 2 by THE PURE DIAMOND πŸ’Ž

SongGPT
Kuwala Kwako (Your Light) 2 by THE PURE DIAMOND πŸ’Ž - Afrobeat music cover art

Kuwala Kwako (Your Light) 2

Afrobeat

0:004:29
Lyrics
Description

[Verse 1] I am alone, I need someone whom can I love, and I need the lonely one, someone who's lovely one, and the one who have good manners, so just because long time is over to survey someone who love me forever at the end I get you babe, kaduwa konga dzuwa ka girl konga ngelo so that babe listen to me concerning my my love πŸ’• yeah!!! babe ndikuuze zakukhosi kwanga, nkanda oyera mukhosi ndinavala, ndipo ndapirira kwa nthawi yayitali, pirira osasirira zambiri, awo ndi mawu omwe agogo ananena, pamapeto ndapezawe kang'enge kaduwa konga dzuwa ka girl konga ngelo , ndikakuona ndimadzala ndi chimwemwe makamaka ukandimweturira, ine ndimangovina uku ndikuufila osati kumangolira kukhala ngati Villa. [Chorus] Kuwala kwako, Chikondi chako, Kukongola kwako, babe umakwana. Kuwala kwako, Chikondi chako, Kukongola kwako, babe umakwana . wandiphwanyira mtima paiwe, my love πŸ’• never end.... nzakukonda mpaka muyaya. wandiphwanyira mtima paiwe, my love πŸ’• never end.... nzakukonda mpaka muyaya . Kuwala kwako, Chikondi chako, Kukongola kwako, babe umakwana. [Verse 2] Konse ndingayende ndiganiza za iwe, even kogona komwe ndikungolota zaiwe, chikondi changa chonse babe chili paiwe, malingaliro anga onse babe ali pa iwe, mtima wanga onse uli pa iwe ndipo ndikonda chabe kuti nawe ukhale waine, chikondi chako chonse babe chikhale paine, malingaliro ako onse babe akhale pa ine, mtima wako onse babe ukhale pa ine ndi moyo wako onse babe ukhale pa ine, ngati uvomera kukhala nane limodzi, ndizakukonda monga nthupi limodzi, ndikupanga umodzi, umodzi wachikondi, mu dziko limodzi, mwafuko limodzi, ndiwe kaduwa samire pa chifuwa ndizimverere kuzuna poti ndiwe mpenda dzuwa , the one thing what I know, babe ndiwe wekha, uyenera kudekha poti! [Chorus] Kuwala kwako, Chikondi chako, Kukongola kwako, babe umakwana. Kuwala kwako, Chikondi chako, Kukongola kwako, babe umakwana . wandiphwanyira mtima paiwe, my love πŸ’• never end.... nzakukonda mpaka muyaya. wandiphwanyira mtima paiwe, my love πŸ’• never end.... nzakukonda mpaka muyaya . Kuwala kwako, Chikondi chako, Kukongola kwako, babe umakwana [Verse 3] Babe imva mawu anga ochoka mkamwa mwanga, sikuti ndine bwana kapena mwana wa bwana, ndiposo ndine nfana ndilibeso ndalama, izi ndimangopanga poti ndili ndi khama, sikuti nkhamba kamwa zimene ndikukamba poti sizifunika kuzitenga maso m'mwamba, if you start uzayamba kuzigamba, apo zitakukhamba kumatiso bola fada Kuti undifunse izi sinangoyamba, panali zambiri zomweso zinandikhamba, but one thing what I know ndikulimba mtima ndichifukwa lero lover ali owina [Chorus] Kuwala kwako, Chikondi chako, Kukongola kwako, babe umakwana. Kuwala kwako, Chikondi chako, Kukongola kwako, babe umakwana . wandiphwanyira mtima paiwe, my love πŸ’• never end.... nzakukonda mpaka muyaya. wandiphwanyira mtima paiwe, my love πŸ’• never end.... nzakukonda mpaka muyaya . Kuwala kwako, Chikondi chako, Kukongola kwako, babe umakwana