Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Kambewa's Anthem 2 by mayamiko

SongGPT
Kambewa's Anthem 2 by mayamiko - Folk-Rock,both vocals music cover art

Kambewa's Anthem 2

Folk-Rock,both vocals

0:003:39
Lyrics
Description
(verse)
pa zambirizo anthu Aku Lumbadzi tionetsetse.
ma shadow ndi onse koma sankhani kolite. Zinazo ndizinyatsi zosadziwa kanthu koma sankhani Mayamiko Kambewa.
yu Ali ndi mzeru zakuya, iye akutumikirani bwino.
abweretsa madzi abwino Kwa onse, adzalimbikitsa masewera onse, Mpira wamiyendo, wamanja ndi zina.
musakaike, kasankheni nyali, nyali ndiye kuunika kwenikweni pa chitukuko.
sankhani Kambewa, Kambewa morefire
(chrous)
tonse tikavotere Kambewa, Kambewa ndi more fire.
mnyamata wachitukuko.
amai ndi abambo munthu ndi Kambewa.
osalakwitsa chizindikiro ndi nyali.
(verse)
kambewa Ali ndi experience, chitukuko amachidziwa
mnyamata oganiza mwa kuya, uyu ndi katswiri
mnyamata wanyamula nyali, kuti anthu onse awone inde awunikiridwe za chitukuko.
mukakafika movotamo kaoneni Pali nyali, voti yanu ili pa nyali
(chrous)
tonse tikavotere Kambewa, Kambewa ndi morefire.
mnyamata wachitukuko.
amai ndi abambo munthu ndi Kambewa.
osalakwitsa chizindikiro ndi nyali.
(bridge)
Lumbadzi yonse, uko Ku mgalamula, inu akwa dzoole uko, osaiwala Kwa katola
uko Kwachepa
konse Kwa maenje
mzikiti yonse, osaiwala mpenda ndi chonveka komaso kawere
(chrous)
tonse tikavotere Kambewa, Kambewa ndi more fire.
mnyamata wachitukuko.
amai ndi abambo munthu ndi Kambewa.
osalakwitsa chizindikiro ndi nyali.