Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Kambewa for Change 2 by mayamiko

SongGPT
Kambewa for Change 2 by mayamiko - Folk-Rock,both vocals music cover art

Kambewa for Change 2

Folk-Rock,both vocals

0:003:44
Lyrics
Description
(verse)
pa zambirizo anthu Aku Lumbadzi tionetsetse.
ma shadow ndi onse koma sankhani kolite.
sankhani Mayamiko Kambewa.
uyu Ali ndi mzeru zakuya, iye akutumikirani bwino.
abweretsa madzi abwino Kwa onse,
adzalimbikitsa masewera onse, Mpira wamiyendo, wamanja ndi zina.
musakaike, kasankheni nyali, nyali ndiye kuunika kwenikweni pa chitukuko.
sankhani Kambewa, Kambewa more fire
(chorus)
tonse tikavotere Kambewa, Kambewa ndi more fire.
mnyamata wachitukuko.
amai ndi abambo munthu ndi Kambewa.
osalakwitsa chizindikiro ndi nyali.
(verse)
kambewa Ali ndi experiment, chitukuko amachidziwa
mnyamata oganiza mwa kuya, uyu ndi katswiri
mnyamata wanyamula nyali, kuti anthu onse awone inde awunikiridwe za chitukuko.
mukakafima movotamo kaoneni Pali nyali
(chorus)
tonse tikavotere Kambewa, Kambewa ndi more fire.
mnyamata wachitukuko.
amai ndi abambo munthu ndi Kambewa.
osalakwitsa chizindikiro ndi nyali.
(bridge)
Lumbadzi yonse, uko Ku mgalamula, inu akwa dzoole uko, osaiwala Kwa katola
uko Kwachepa
konse Kwa maenje
mzikiti yonse, osaila mpenda ndi chonveka
(chrous)
tonse tikavotere Kambewa, Kambewa ndi more fire.
mnyamata wachitukuko.
amai ndi abambo munthu ndi Kambewa.
osalakwitsa chizindikiro ndi nyali.