Famaju mw (mundisiye ndekha) 2 by Alufandika

SongGPT
Famaju mw (mundisiye ndekha) 2 by Alufandika - Amapiano music cover art

Famaju mw (mundisiye ndekha) 2

Alufandika

Amapiano

0:002:58
Lyrics
Description
[Intro]
mmmmm Famaju Malawi
eeeeeee iiiiiik Famaju
[Chorus]
mundisiye ndekha mundisiye ndekha ine eeeeeeee
mundisiye ndekha mundisiye ndekha ine
[Verse 1]
mmmmm ndimkakudalira ine kuti ndidzakhara nawe ine
eeee koma osadziwa kuti ndiwe hule iwe eeee
ukandiuza ngati chikondi chimachepa mwina mkanaonjezera ine
mmmm Famaju Malawi
[Chorus]
mundisiye ndekha mundisiye ndekha ine eeeeeeee
mundisiye ndekha mundisiye ndekha ine eeeeeeee
[Verse 2]
pano ndikulira ndikaganizira ndalama yanga zalowa madzi
salary ikalowa ndimkakugulira zodura kuti uware mkazi koma ndikamadziwa mkanakusiya pachiyambi mphuno salota Famaju wamusiyira mabala mumtima mwanga
[Chorus]
mundisiye ndekha mundisiye ndekha ine eeeeeeee
mundisiye ndekha mundisiye ndekha ine eeeeeeee
[Verse 3]
pitani tidzaonana amoyo salekana ndine amene ndinakuchoka uchimidzi koma chongokutenga unachapika maso pamawa udzandifuna ine mwawina ndinu ine opusa mmmmmm Famaju Malawi
[Outro]
mundisiye ndekha mundisiye ndekha ine eeeeeeee
mundisiye ndekha mundisiye ndekha ine