Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Famaju mw (Love Yamufilimu) 1 by Alufandika

SongGPT
Famaju mw (Love Yamufilimu) 1 by Alufandika - trap music cover art

Famaju mw (Love Yamufilimu) 1

trap

0:003:02
Lyrics
Description
[Intro]
mmmmmm Famaju Malawi
[Chorus]
Mami undikonde ngati love yamufilimu
Mami undikonde ngati love yamufilimu
ndilinawe mpaka forever
[Verse 1]
Famaju bebi tiyende limodzi mpaka tikafike olewa ndiambiri aleke anene
Mami usayang'ane mbuyo ngati mkazi wa loti . bebi tiyende limodzi mpaka tikafike olewa ndiambiri aleke anene
[Chorus]
Mami undikonde ngati love yamufilimu
Mami undikonde ngati love yamufilimu
ndilinawe mpaka forever
[Verse 2]
bebi give me love ayi give the same
don't live me alone ndilinawe mpaka forever
mkazi bwera tivine limodzi mmmmm bebi vina vina tsika gwedeza nyashi
[Verse 3]
tikondane mene achitira biyonse ndi akila
nditengere kwanu akandidziwe kuti ndine amene dzakusamare tiye kwathu akakudziwe kuti ndiwe amene unandibera mtima wanga mmmmmm Famaju Malawi
[Outro]
mmmmmm Famaju Malawi