Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Chuma Chamakolo 2 by Phude

SongGPT
Chuma Chamakolo 2 by Phude - Afrobeat music cover art

Chuma Chamakolo 2

Afrobeat

0:002:59
Lyrics
Description
[Intro]
Ah, Katchale
Chuma chamakolo
Eeeh, mwandivetsa?
[Verse 1]
Anapusitsidwa ndi chuma chamakolo
Kumangonjoya, kumangonjoya basi
Osapanga lawo, tsogolo anayiwalira
Makolo anali ndi zonse, iye anangodya zokoma
Anayiwalira kuti mone is tail of mouse
Ukapanda kugwilira bwino umapululuka
Analibe nzeru, analibe maganizo
Chuma chonse chinali m'manja mwake
[Pre-Chorus]
Koma lero, lero ndi lero
Chuma chija chinatha, chinatha basi
Makolo awo ifa inawatenga
Alibe kanthu, alibe munthu
[Chorus]
Chuma chamakolo, chinatha
Makolo awo ifa inawatenga
Opanga support amasowa
Amangolira maka akakumbika mmene kunalili kwawo
Chuma chamakolo, chinatha
Mone is tail of mouse, umapululuka
Lero opanga support amasowa
Amangolira, amangolira
[Verse 2]
Pano ali yekha, palibe wina
Nyumba yaikulu ija, yagwa
Galimoto zija, zinathengedwa
Ndalama zija, zinapita ku bar, ku club
Anzake anali ambiri pamene anali ndi chuma
Koma lero, lero palibe ndi mmodzi
Akakumbuka masiku akale
Misozi ikungotuluka, ikungotuluka
[Pre-Chorus]
Koma lero, lero ndi lero
Chuma chija chinatha, chinatha basi
Makolo awo ifa inawatenga
Alibe kanthu, alibe munthu
[Chorus]
Chuma chamakolo, chinatha
Makolo awo ifa inawatenga
Opanga support amasowa
Amangolira maka akakumbika mmene kunalili kwawo
Chuma chamakolo, chinatha
Mone is tail of mouse, umapululuka
Lero opanga support amasowa
Amangolira, amangolira
[Bridge]
Tsogolo, tsogolo, anayiwalira
Kusangalala basi, kusangalala
Koma mone is tail of mouse
Ukapanda kugwilira bwino
Umapululuka, umapululuka
Chuma chamakolo sichimakhala chonse
Uyenera kupanga lako, kupanga lako
[Chorus]
Chuma chamakolo, chinatha
Makolo awo ifa inawatenga
Opanga support amasowa
Amangolira maka akakumbika mmene kunalili kwawo
Chuma chamakolo, chinatha
Mone is tail of mouse, umapululuka
Lero opanga support amasowa
Amangolira, amangolira
[Outro]
Mmene kunalili kwawo
Mmene kunalili kwawo
Koma lero, palibe kanthu
Chuma chamakolo... chinatha