Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Chikondi Wanga 1 by Mahowa

SongGPT
Chikondi Wanga 1 by Mahowa - afrobeat,female vocals music cover art

Chikondi Wanga 1

afrobeat,female vocals

0:003:16
Lyrics
Description
Verse 1:
mmm mmmm mmmmm mm
chikondi wanga , nkanzi wanga , uli ndine mahowa ndimakukonda.
Verse 2:
chikondi, chikondi ine ndimakukondaa
nthawi zonse ndimakuganizira .
tidzakhale limodzi iwe ndine mpaka muyaya ah, moyo wanga uli mmanja mwa iwe.
Chorus:
chikondi chikondi ine ndimakukondaa, ndikakhala ndi iwe moyo wanga umasangalala, nthawi zonse ine ndimakuganizira,chikondi changa ndapelekaa kwa iwe oh mm
Verse 3:
iwe chikondi dziwa kuti ndimakukondaa, popanda iwe moyo wanga uli chabe,
dizakukonda moyo wanga wonse chifukwa iwe , watenga mtima wanga
mmm mmm chikondi I love youu
Bridge:
mmm mmmm yee , chikondi chikondi ine ndimakukondaa popanda iwe moyo wanga uli chabe , tabwera pafuna, ndipo undi hode nane, uyende chifupi nane chikondi iwe yee
Outro:
mmmm mmmm m yee