Create New Playlist

Add a cover pic of your own choice

(Optional)

Name

AI Cover Generator

4 credits

Not enough credits (0/4).

Logout

Are you sure you want to Logout?

Close

Am Nothing Without You 1 by Peter

SongGPT
Am Nothing Without You 1 by Peter - Afrobeat, World Music,Neutral Vocals music cover art

Am Nothing Without You 1

Afrobeat, World Music,Neutral Vocals

0:003:09
Lyrics
Description
[Intro]
Amatchenyanga pachikaya tiyende limodzi
[Chorus]
Am nothing without you
Mtima Kuwawa
Chimwemwe kutsowa mtendere kuthawa
Am nothing without you
Aaaah without you
[Verse]
Time
Dear ndakutsowa moyo opanda iwe ukuchita kubhowa
Kutsowa pokhala ndingokhalila mowa
My life is empty opanda iweyo
Am lost in the mountain
Mulanje chamkati mkati
Ndikufuna iwe apa ndikutsala kudya
Ndafooka ndiponyere chingwe
I wanna be with you
[Chorus]
Am nothing without you
Mtima Kuwawa
Chimwemwe kutsowa mtendere kuthawa
Am nothing without you
Aaaah without you
Oooh
[Verse]
Tonse limodzi chikondi chokoma
Tonse ndi Amalawi ili lathu boma
With you chitukuko pa boma
Mtendere mtima
Am with you darling
Oh oh Mai malawi
[Bridge]
Come on
Tiye tivine
Darling nana nana
[Chorus]
Am nothing without you
Mtima Kuwawa
Chimwemwe kutsowa mtendere kuthawa
Am nothing without you
Aaaah without you
Oooh